MACRA COMMEMORATES SAFER INTERNET DAY
Bungwe la MACRA mothandizana ndi a Youth Net Counselling (YONECO) alangiza zakufunikira kogwirana manja poonetsetsa kuti ana ali otetezeka pamene akugwiritsa ntchito intaneti. Izi zinakambidwa pa sukulu ya Zomba Catholic Secondary pamwambo okumbukira malo otetezeka pa intaneti padziko lonse, womwe umakumbukiridwa pa 2 February chaka chilichonse, ndipo dziko la Malawi likuchita mwambowu kuyambira pa 23 […]
MACRA COMMEMORATES SAFER INTERNET DAY Read More »









